1 Mafumu 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iweyo uchite zinthu mogwirizana ndi nzeru zako ndipo usalole kuti imvi zake zidzapite ku Manda* mwamtendere.+
6 Iweyo uchite zinthu mogwirizana ndi nzeru zako ndipo usalole kuti imvi zake zidzapite ku Manda* mwamtendere.+