1 Mafumu 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ana a Barizilai+ wa ku Giliyadi uwasonyeze chikondi chokhulupirika. Akhale mʼgulu la anthu amene azidya patebulo lako, chifukwa anandithandiza+ pa nthawi imene ndinkathawa mchimwene wako Abisalomu.+
7 Koma ana a Barizilai+ wa ku Giliyadi uwasonyeze chikondi chokhulupirika. Akhale mʼgulu la anthu amene azidya patebulo lako, chifukwa anandithandiza+ pa nthawi imene ndinkathawa mchimwene wako Abisalomu.+