1 Mafumu 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iweyo usangomusiya, umulange,+ poti ndiwe munthu wanzeru ndipo ukudziwa zimene uyenera kumuchita. Uchite zoti imvi zake zipite ku Manda* zili ndi magazi.”+
9 Iweyo usangomusiya, umulange,+ poti ndiwe munthu wanzeru ndipo ukudziwa zimene uyenera kumuchita. Uchite zoti imvi zake zipite ku Manda* zili ndi magazi.”+