1 Mafumu 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Solomo anakhala pampando wachifumu wa Davide bambo ake, ndipo patapita nthawi ufumu wake unakhazikika.+
12 Ndiyeno Solomo anakhala pampando wachifumu wa Davide bambo ake, ndipo patapita nthawi ufumu wake unakhazikika.+