-
1 Mafumu 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako Adoniya mwana wa Hagiti anapita kwa Bati-seba, amayi ake a Solomo ndipo iwo anamufunsa kuti: “Kodi nʼkwabwino?” Iye anayankha kuti: “Inde, nʼkwabwino.”
-