1 Mafumu 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Adoniya anati: “Chonde, mukapemphe Mfumu Solomo kuti andipatse Abisagi+ wa ku Sunemu kuti akhale mkazi wanga. Ndikudziwa kuti inuyo sakakukanirani.” 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:17 Nsanja ya Olonda,7/1/2005, tsa. 29
17 Kenako Adoniya anati: “Chonde, mukapemphe Mfumu Solomo kuti andipatse Abisagi+ wa ku Sunemu kuti akhale mkazi wanga. Ndikudziwa kuti inuyo sakakukanirani.”