-
1 Mafumu 2:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndiyeno Bati-seba anati: “Pali chinthu chachingʼono chimodzi chimene ndikufuna kupempha. Chonde musandikanire.” Mfumuyo inati: “Pemphani amayi, sindikukanirani.”
-