-
1 Mafumu 2:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Kenako Mfumu Solomo analumbira pamaso pa Yehova kuti: “Mulungu andilange mowirikiza ngati Adoniya sanaike moyo wake pangozi popempha zimenezi.
-