1 Mafumu 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho Solomo anachotsa Abiyatara kuti asatumikirenso monga wansembe wa Yehova ndipo izi zinakwaniritsa mawu amene Yehova analankhula ku Silo+ okhudza nyumba ya Eli.+
27 Choncho Solomo anachotsa Abiyatara kuti asatumikirenso monga wansembe wa Yehova ndipo izi zinakwaniritsa mawu amene Yehova analankhula ku Silo+ okhudza nyumba ya Eli.+