1 Mafumu 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yowabu atamva za nkhaniyi, anathawira kuchihema cha Yehova+ nʼkukagwira nyanga za guwa lansembe. Paja Yowabu ankatsatira Adoniya,+ koma sanatsatire Abisalomu.+
28 Yowabu atamva za nkhaniyi, anathawira kuchihema cha Yehova+ nʼkukagwira nyanga za guwa lansembe. Paja Yowabu ankatsatira Adoniya,+ koma sanatsatire Abisalomu.+