1 Mafumu 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mfumuyo inamuuza kuti: “Chita zimene wakuuzazo. Ukamuphe nʼkumuika mʼmanda ndipo undichotsere ineyo komanso nyumba ya bambo anga magazi amene Yowabu anakhetsa popanda chifukwa.+
31 Mfumuyo inamuuza kuti: “Chita zimene wakuuzazo. Ukamuphe nʼkumuika mʼmanda ndipo undichotsere ineyo komanso nyumba ya bambo anga magazi amene Yowabu anakhetsa popanda chifukwa.+