-
1 Mafumu 2:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Yehova adzachititsa kuti magazi ake akhale pamutu pake, chifukwa anapha ndi lupanga anthu awiri olungama komanso abwino kuposa iyeyo. Anachita zimenezi Davide bambo anga osadziwa. Iye anapha Abineri+ mwana wa Nera mkulu wa asilikali a Isiraeli+ ndiponso Amasa+ mwana wa Yeteri mkulu wa asilikali a Yuda.+
-