1 Mafumu 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako mfumu inaitanitsa Simeyi+ nʼkumuuza kuti: “Umange nyumba yako ku Yerusalemu ndipo uzikhala kumeneko. Usadzachokeko nʼkupita kwina kulikonse.
36 Kenako mfumu inaitanitsa Simeyi+ nʼkumuuza kuti: “Umange nyumba yako ku Yerusalemu ndipo uzikhala kumeneko. Usadzachokeko nʼkupita kwina kulikonse.