1 Mafumu 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsiku limene udzachoke nʼkudutsa chigwa cha Kidironi,+ udziwiretu kuti udzafa. Mlandu wa magazi ako udzakhala pamutu pako.”
37 Tsiku limene udzachoke nʼkudutsa chigwa cha Kidironi,+ udziwiretu kuti udzafa. Mlandu wa magazi ako udzakhala pamutu pako.”