1 Mafumu 2:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma patatha zaka zitatu, akapolo awiri a Simeyi anathawira kwa Akisi+ mwana wa Maaka, mfumu ya ku Gati. Kenako Simeyi anauzidwa kuti: “Akapolo anutu ali ku Gati.”
39 Koma patatha zaka zitatu, akapolo awiri a Simeyi anathawira kwa Akisi+ mwana wa Maaka, mfumu ya ku Gati. Kenako Simeyi anauzidwa kuti: “Akapolo anutu ali ku Gati.”