1 Mafumu 2:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Kenako mfumuyo inauza Simeyi kuti: “Iweyo ukudziwa mumtima mwako zoipa zonse zimene unachitira Davide bambo anga.+ Yehova akubwezera pamutu pako zoipa zimene unachita.+
44 Kenako mfumuyo inauza Simeyi kuti: “Iweyo ukudziwa mumtima mwako zoipa zonse zimene unachitira Davide bambo anga.+ Yehova akubwezera pamutu pako zoipa zimene unachita.+