1 Mafumu 2:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndiyeno mfumuyo inalamula Benaya mwana wa Yehoyada kuti aphe Simeyi ndipo anamuphadi.+ Choncho ufumu unakhazikika mʼmanja mwa Solomo.+
46 Ndiyeno mfumuyo inalamula Benaya mwana wa Yehoyada kuti aphe Simeyi ndipo anamuphadi.+ Choncho ufumu unakhazikika mʼmanja mwa Solomo.+