1 Mafumu 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumu inapita ku Gibiyoni kukapereka nsembe, chifukwa kumeneko nʼkumene kunali malo okwezeka otchuka* kwambiri.+ Solomo anapereka nsembe zopsereza zokwana 1,000 paguwa lansembe.+
4 Mfumu inapita ku Gibiyoni kukapereka nsembe, chifukwa kumeneko nʼkumene kunali malo okwezeka otchuka* kwambiri.+ Solomo anapereka nsembe zopsereza zokwana 1,000 paguwa lansembe.+