1 Mafumu 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Mulungu anamuuza kuti: “Popeza wapempha zimenezi ndipo sunapemphe moyo wautali, chuma, kapena kuti adani ako afe, koma wapempha kuti ukhale womvetsa zinthu kuti uzitha kuweruza milandu,+
11 Ndiyeno Mulungu anamuuza kuti: “Popeza wapempha zimenezi ndipo sunapemphe moyo wautali, chuma, kapena kuti adani ako afe, koma wapempha kuti ukhale womvetsa zinthu kuti uzitha kuweruza milandu,+