1 Mafumu 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ndikupatsa zimene wapempha.+ Ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ kuposa anthu onse amene anakhalapo mʼmbuyomu komanso amene adzakhaleko mʼtsogolo.+
12 ndikupatsa zimene wapempha.+ Ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ kuposa anthu onse amene anakhalapo mʼmbuyomu komanso amene adzakhaleko mʼtsogolo.+