1 Mafumu 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo ukamayenda mʼnjira zanga posunga malangizo ndi malamulo anga ngati mmene Davide bambo ako anachitira,+ ndidzakupatsanso moyo wautali.”+
14 Ndipo ukamayenda mʼnjira zanga posunga malangizo ndi malamulo anga ngati mmene Davide bambo ako anachitira,+ ndidzakupatsanso moyo wautali.”+