-
1 Mafumu 3:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mkazi mmodzi anati: “Mbuyanga, ine ndi mayi uyu tikukhala mʼnyumba imodzi. Ndipo ine ndinabereka mwana wamwamuna iyeyu ali mʼnyumba momwemo.
-