-
1 Mafumu 3:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Nthawi yomweyo mayi yemwe mwana wake anali wamoyoyo anayamba kuchonderera mfumu chifukwa chochitira chifundo mwana wakeyo. Iye anauza mfumuyo kuti: “Chonde mbuyanga, mʼpatseni mayiyu mwana wamoyoyu. Musamuphe.” Koma mayi winayo ankanena kuti: “Mwana ameneyu sakhala wanga kapena wako. Amudule pakati basi!”
-