1 Mafumu 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Aisiraeli onse anamva mmene mfumu inaweruzira nkhaniyo ndipo anachita mantha ndi mfumuyo+ chifukwa anaona kuti Mulungu wamupatsa nzeru kuti aziweruza mwachilungamo.+
28 Aisiraeli onse anamva mmene mfumu inaweruzira nkhaniyo ndipo anachita mantha ndi mfumuyo+ chifukwa anaona kuti Mulungu wamupatsa nzeru kuti aziweruza mwachilungamo.+