1 Mafumu 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo anthu amene anali ndi maudindo ndi awa: Azariya mwana wa Zadoki anali wansembe.+