1 Mafumu 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Benaya+ mwana wa Yehoyada anali mkulu wa asilikali, ndipo Zadoki ndi Abiyatara+ anali ansembe.