1 Mafumu 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Solomo anali ndi nduna 12 zomwe zinkayangʼanira Aisiraeli onse ndipo zinkabweretsa chakudya kwa mfumu ndi banja lake. Nduna iliyonse inkabweretsa chakudya kwa mwezi umodzi pachaka.+
7 Solomo anali ndi nduna 12 zomwe zinkayangʼanira Aisiraeli onse ndipo zinkabweretsa chakudya kwa mfumu ndi banja lake. Nduna iliyonse inkabweretsa chakudya kwa mwezi umodzi pachaka.+