1 Mafumu 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Baana mwana wa Ahiludi ankayangʼanira ku Taanaki, ku Megido+ ndi ku Beti-seani+ konse, pafupi ndi Zeretani kumunsi kwa Yezereeli, kuchokera ku Beti-seani kukafika ku Abele-mehola mpaka kuchigawo cha Yokimeamu.+
12 Baana mwana wa Ahiludi ankayangʼanira ku Taanaki, ku Megido+ ndi ku Beti-seani+ konse, pafupi ndi Zeretani kumunsi kwa Yezereeli, kuchokera ku Beti-seani kukafika ku Abele-mehola mpaka kuchigawo cha Yokimeamu.+