1 Mafumu 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye ankalamulira chilichonse kumbali yakumadzulo kwa Mtsinje,*+ kuchokera ku Tifisa mpaka ku Gaza.+ Ankalamulira mafumu onse a mbali yakumadzulo kwa Mtsinje ndipo mʼzigawo zake zonse munali mtendere.+
24 Iye ankalamulira chilichonse kumbali yakumadzulo kwa Mtsinje,*+ kuchokera ku Tifisa mpaka ku Gaza.+ Ankalamulira mafumu onse a mbali yakumadzulo kwa Mtsinje ndipo mʼzigawo zake zonse munali mtendere.+