1 Mafumu 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iye anali wanzeru kuposa munthu aliyense. Anali wanzeru kuposa Etani+ mbadwa ya Zera ndiponso Hemani,+ Kalikoli+ ndi Darida ana a Maholi moti anatchuka mʼmitundu yonse yozungulira.+
31 Iye anali wanzeru kuposa munthu aliyense. Anali wanzeru kuposa Etani+ mbadwa ya Zera ndiponso Hemani,+ Kalikoli+ ndi Darida ana a Maholi moti anatchuka mʼmitundu yonse yozungulira.+