1 Mafumu 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Hiramu, mfumu ya ku Turo,+ atamva kuti Solomo wadzozedwa kukhala mfumu mʼmalo mwa bambo ake, anatuma atumiki ake kuti apite kwa Solomo popeza Hiramuyo anali mnzake wa Davide.+
5 Hiramu, mfumu ya ku Turo,+ atamva kuti Solomo wadzozedwa kukhala mfumu mʼmalo mwa bambo ake, anatuma atumiki ake kuti apite kwa Solomo popeza Hiramuyo anali mnzake wa Davide.+