1 Mafumu 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inuyo mukudziwa bwino kuti Davide bambo anga sanathe kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wake, chifukwa cha nkhondo zimene adani ake ankamenyana naye mʼmadera onse omuzungulira, mpaka pamene Yehova anamuthandiza kugonjetsa adani akewo.*+
3 “Inuyo mukudziwa bwino kuti Davide bambo anga sanathe kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wake, chifukwa cha nkhondo zimene adani ake ankamenyana naye mʼmadera onse omuzungulira, mpaka pamene Yehova anamuthandiza kugonjetsa adani akewo.*+