1 Mafumu 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma panopa Yehova Mulungu wanga wandipatsa mpumulo moti adani anga onse ondizungulira sakumenyana nane.+ Palibe aliyense amene akulimbana nane komanso palibe choipa chilichonse chimene chikuchitika.+
4 Koma panopa Yehova Mulungu wanga wandipatsa mpumulo moti adani anga onse ondizungulira sakumenyana nane.+ Palibe aliyense amene akulimbana nane komanso palibe choipa chilichonse chimene chikuchitika.+