5 Choncho ndikuganiza zomanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wanga, mogwirizana ndi zimene Yehova analonjeza Davide bambo anga kuti, ‘Mwana wako amene ndidzamuike pampando wako wachifumu mʼmalo mwa iweyo, ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.’+