1 Mafumu 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Hiramu atamva zimene Solomo ananenazi, anasangalala kwambiri ndipo anati: “Yehova atamandike lero chifukwa wapereka kwa Davide mwana wanzeru woti alamulire anthu ochulukawa.”+
7 Hiramu atamva zimene Solomo ananenazi, anasangalala kwambiri ndipo anati: “Yehova atamandike lero chifukwa wapereka kwa Davide mwana wanzeru woti alamulire anthu ochulukawa.”+