1 Mafumu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Hiramu anatumiza uthenga kwa Solomo wakuti: “Ndamva uthenga wanu. Ndichita zonse zimene mukufuna ndipo ndikupatsani mitengo ya mkungudza ndiponso mitengo ya junipa.*+
8 Choncho Hiramu anatumiza uthenga kwa Solomo wakuti: “Ndamva uthenga wanu. Ndichita zonse zimene mukufuna ndipo ndikupatsani mitengo ya mkungudza ndiponso mitengo ya junipa.*+