1 Mafumu 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Yehova anapatsa Solomo nzeru mogwirizana ndi zimene anamulonjeza.+ Pakati pa Hiramu ndi Solomo panali mtendere ndipo awiriwa anachita pangano.
12 Ndiyeno Yehova anapatsa Solomo nzeru mogwirizana ndi zimene anamulonjeza.+ Pakati pa Hiramu ndi Solomo panali mtendere ndipo awiriwa anachita pangano.