1 Mafumu 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inkawatumiza ku Lebanoni mʼmagulu a anthu 10,000 pamwezi. Anthuwo ankakhala mwezi umodzi ku Lebanoni ndipo miyezi iwiri ankakhala kwawo. Adoniramu+ ndi amene ankayangʼanira anthu ogwira ntchito yokakamizawo.
14 Inkawatumiza ku Lebanoni mʼmagulu a anthu 10,000 pamwezi. Anthuwo ankakhala mwezi umodzi ku Lebanoni ndipo miyezi iwiri ankakhala kwawo. Adoniramu+ ndi amene ankayangʼanira anthu ogwira ntchito yokakamizawo.