1 Mafumu 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Solomo anali ndi anthu 70,000 onyamula katundu ndiponso anthu 80,000 osema miyala+ kumapiri.+