1 Mafumu 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova*+ mʼchaka cha 480 kuchokera pamene Aisiraeli anatuluka mʼdziko la Iguputo,+ mwezi wa Zivi*+ (womwe ndi mwezi wachiwiri). Ichi chinali chaka cha 4 kuchokera pamene Solomoyo anakhala mfumu ya Isiraeli. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:1 Galamukani!,5/2012, tsa. 17
6 Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova*+ mʼchaka cha 480 kuchokera pamene Aisiraeli anatuluka mʼdziko la Iguputo,+ mwezi wa Zivi*+ (womwe ndi mwezi wachiwiri). Ichi chinali chaka cha 4 kuchokera pamene Solomoyo anakhala mfumu ya Isiraeli.