1 Mafumu 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso anamanga zipinda kuzungulira khoma lonse la nyumbayo, kuzungulira makoma onse akunja a kachisi* ndi chipinda chamkati.+ Anamanganso zipinda zamʼmbali zosanjikizana kuzungulira nyumbayo.+
5 Komanso anamanga zipinda kuzungulira khoma lonse la nyumbayo, kuzungulira makoma onse akunja a kachisi* ndi chipinda chamkati.+ Anamanganso zipinda zamʼmbali zosanjikizana kuzungulira nyumbayo.+