1 Mafumu 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chipinda chamʼmbali chapansi chinali mikono 5 mulifupi mwake, chapakati chinali mikono 6 mulifupi mwake ndipo chachitatu chinali mikono 7 mulifupi mwake. Makoma onse akunja a nyumbayo anangowagoba nʼcholinga choti asawaboole.+
6 Chipinda chamʼmbali chapansi chinali mikono 5 mulifupi mwake, chapakati chinali mikono 6 mulifupi mwake ndipo chachitatu chinali mikono 7 mulifupi mwake. Makoma onse akunja a nyumbayo anangowagoba nʼcholinga choti asawaboole.+