1 Mafumu 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyumbayo anaimanga ndi miyala yosema kale,+ ndipo phokoso la hamala, nkhwangwa kapena zida zilizonse zachitsulo silinkamveka pamene ankaimanga.
7 Nyumbayo anaimanga ndi miyala yosema kale,+ ndipo phokoso la hamala, nkhwangwa kapena zida zilizonse zachitsulo silinkamveka pamene ankaimanga.