1 Mafumu 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anagawanso chipinda cha mikono 20 kumbuyo kwa nyumbayo pogwiritsa ntchito matabwa akuluakulu a mkungudza, kuchokera pansi mpaka kudenga. Ndipo mʼchipindamo anamangamo chipinda chamkati+ chotchedwa Malo Oyera Koposa.+
16 Anagawanso chipinda cha mikono 20 kumbuyo kwa nyumbayo pogwiritsa ntchito matabwa akuluakulu a mkungudza, kuchokera pansi mpaka kudenga. Ndipo mʼchipindamo anamangamo chipinda chamkati+ chotchedwa Malo Oyera Koposa.+