1 Mafumu 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chipinda chamkaticho chinali mikono 20 mulitali, mikono 20 mulifupi ndi mikono 20 kupita mʼmwamba.+ Chipindachi anachikuta ndi golide woyenga bwino, komanso anakuta guwa lansembe+ ndi matabwa a mkungudza.
20 Chipinda chamkaticho chinali mikono 20 mulitali, mikono 20 mulifupi ndi mikono 20 kupita mʼmwamba.+ Chipindachi anachikuta ndi golide woyenga bwino, komanso anakuta guwa lansembe+ ndi matabwa a mkungudza.