1 Mafumu 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nyumba yonseyo anaikuta ndi golide mpaka kuimaliza, ndipo guwa lansembe lonse, lomwe linali pafupi ndi chipinda chamkati, analikuta ndi golide.+
22 Nyumba yonseyo anaikuta ndi golide mpaka kuimaliza, ndipo guwa lansembe lonse, lomwe linali pafupi ndi chipinda chamkati, analikuta ndi golide.+