1 Mafumu 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mʼchipinda chamkati Solomo anapangamo akerubi awiri+ pogwiritsa ntchito mtengo wa paini.* Kerubi aliyense anali wamtali mikono 10.+
23 Mʼchipinda chamkati Solomo anapangamo akerubi awiri+ pogwiritsa ntchito mtengo wa paini.* Kerubi aliyense anali wamtali mikono 10.+