1 Mafumu 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako akerubiwo+ anawaika mʼchipinda chamkati.* Mapiko awo anali otambasula moti phiko la kerubi mmodzi linagunda khoma ndipo phiko la kerubi wina linagundanso khoma lina. Mapiko awo anafika pakati pa nyumbayo, ndipo anagundana.
27 Kenako akerubiwo+ anawaika mʼchipinda chamkati.* Mapiko awo anali otambasula moti phiko la kerubi mmodzi linagunda khoma ndipo phiko la kerubi wina linagundanso khoma lina. Mapiko awo anafika pakati pa nyumbayo, ndipo anagundana.