-
1 Mafumu 6:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Zitseko ziwirizo zinali zamatabwa a mtengo wa paini ndipo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mitengo ya kanjedza ndi maluwa. Zitsekozo anazikuta ndi golide. Akerubi ndi mitengo ya kanjedza zomwe anazilemba mochita kugoba pazitsekozo anazikutanso ndi golide.
-