-
1 Mafumu 6:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Anapanga zitseko ziwiri zamatabwa a mitengo yofanana ndi mkungudza. Chitseko choyamba chinali ndi mbali ziwiri ndipo hafu inkatsegukira mbali ina, hafu ina inkatsegukira mbali ina. Chitseko chachiwiri chinalinso ndi mbali ziwiri ndipo hafu inkatsegukira mbali ina, hafu ina inkatsegukira mbali ina.+
-